Dean wa Mtima Woyera Deanery, Bambo Augustine Katundu ati sakramenti la ulimbitso likuyenera kukhala lothandiza achinyamata amene alandira ulimbitso pakutumikira mulungu tsiku ndi tsiku. Bambo Katundu ayankhula izi Loweruka pa 02 September 2023 pambuyo pa mwambo wa sakramenti la ulimbitso omwe achinyamata okwana 97 alandira pa Parish ya St Patricks, mu Arkidayosizi ya Lilongwe. Bambo… Continue reading ACHINYAMATA OKWANA 97 ALANDIRA SAKRAMENTI LA ULIMBITSO PA PARISH YA ST PATRICKS MU ARKIDAYOSIZI YA LILONGWE
ACHINYAMATA OKWANA 97 ALANDIRA SAKRAMENTI LA ULIMBITSO PA PARISH YA ST PATRICKS MU ARKIDAYOSIZI YA LILONGWE
