
AMBUYE TAMBALA APEMPHA ZIPANI ZAMUMPINGO KUFIKIRA ACHINYAMATA KU MAPARISHI AWO
Ambuye George Desmond Tambala, Arkiepiskopi wa Arkidayosizi yaKatolika ya Lilongwe, apempha zipani za ansembe komanso ma sisitele mu arkidayosiziyi kuti afikire achinyamata m’maparishi osiyanasiyana ndi




