
“Achinyamata Asinkhesinkhe za Mayitanidwa Awo; Lero osati mawa,” Ambuye George Tambala
Achinyamata mu Arkidayosizi ya Lilongwe, apemphedwa kuti akuyenera kugwiritsa ntchito mwayi komanso kupanga ziganizo zoyenera pa momwe angatumikire Mulungu kudzera mmayitanidwe awo. Ambuye George Desmond




