New Year Wishes from Our Staff (Mafuno abwino a chaka chatsopano kuchokera kwa ogwira ntchito athu)
As we start this New Year, the staff of Radio Alinafe warmly wish all our listeners, followers, and partners a blessed and fruitful year ahead. We thank you for your continued support and prayers.
Pamene tikuyamba chaka chatsopanochi, ogwira ntchito a Radio Alinafe akupereka mafuno abwino kwa anthu onse omwe amatitsatira. Tikukuthokozani chifukwa cha thandizo lanu ndipo tikupempherani madalitso ochuluka ochokera kwa Mulungu.
Watch here (Onerani kanema wa mafuno abwinoyu apa):