SMALLHOLDER FARMERS CROP DIVERSIFICATION KEY FOR MITIGATING CLIMATE CHANGE SHOCKS

The Vice President and Country Director of the Foundation for a Smoke-Free World, Dr. Candida Nakhumwa says farmers across the country (Malawi) are responding well in-terms of diversifying from relying on Tobacco only as a cash crop to other alternative value chains. Dr. Nakhumwa made the remarks on Wednesday, 24 April 2024 at NRC –… Continue reading SMALLHOLDER FARMERS CROP DIVERSIFICATION KEY FOR MITIGATING CLIMATE CHANGE SHOCKS

DON BOSCO TECH AFRICA LAUNCHES THE COMMUNICATIONS STRATEGY IN MALAWI

Don Bosco Youth Technical Institute has on 22 April 2024 hosted the launch of communication strategy in the country as one of the countries under Don Bosco Tech-Africa. Malawi has become the first country to launch the communication strategy out of the 11 countries which are under the Don Bosco Tech Africa. Speaking at the… Continue reading DON BOSCO TECH AFRICA LAUNCHES THE COMMUNICATIONS STRATEGY IN MALAWI

AMBUYE TAMBALA APEMPHA ZIPANI ZAMUMPINGO KUFIKIRA ACHINYAMATA KU MAPARISHI AWO

Ambuye George Desmond Tambala, Arkiepiskopi wa Arkidayosizi yaKatolika ya Lilongwe, apempha zipani za ansembe komanso ma sisitele mu arkidayosiziyi kuti afikire achinyamata m’maparishi osiyanasiyana ndi cholinga choti azimvetsesa nkhani za mayitanidwe. Ambuye Tambala ayankhula izi la Mulungu la Mayitanidwe, 21 April 2024 ku Parishi ya Mlare pa mwambo wa nsembe ya misa yomwe achinyamata mu… Continue reading AMBUYE TAMBALA APEMPHA ZIPANI ZAMUMPINGO KUFIKIRA ACHINYAMATA KU MAPARISHI AWO

BUNGWE LA CAT LILIMBIKITSA ULIMI WA MAWUNGU AKULUAKULU (GIANT PUMPKINS)

Bungwe la Centre for Agricultural Transformation (CAT) lapempha alimi m’dziko muno kuyamba kubzala mbeu ya maungu akuluakulu (Giant Pumpkins) ndi cholinga chofuna kuchepetsa njala yomwe imakuta dziko lino chaka ndi chaka. Izi zayankhulidwa lachisanu pa 16 February 2024 pamwambo wachionetsero cha mbewu ya mawunguyi, yomwe ikutchedwa NRC Giant Pumpkin, yomwe inalimidwa miyezi ingapo yapitayi ku… Continue reading BUNGWE LA CAT LILIMBIKITSA ULIMI WA MAWUNGU AKULUAKULU (GIANT PUMPKINS)

CHIPANI CHA A SISTERE CHA M.M.M CHAYAMIKILIDWA KAMBA KA NTCHITO ZAKE MU ARKIDAYOSIZI YAKATOLIKA YA LILONGWE

Wolemba ndi Sam Kalimba Arkidayosizi ya Lilongwe yayamikira ndi kulimbikitsa a sistere a chipani cha Missionaries of Mary Mediatrix (M.M.M) kamba ka utumiki wawo womwe ati akuwugwira modziyiwala mu Arkidayosiziyi. Arkiepisikopi wa Arkidayosiziyi George Desmond Tambala ndiwo ayankhula izi pa mbuyo pa mwambo wa Misa ya malumbiro oyamba a Sr. Apronia Mahowe ndi Sr. Stella… Continue reading CHIPANI CHA A SISTERE CHA M.M.M CHAYAMIKILIDWA KAMBA KA NTCHITO ZAKE MU ARKIDAYOSIZI YAKATOLIKA YA LILONGWE

BISHOP MWAKHWAWA ENTREATS THE YOUTH TO RESPOND TO THEIR VOCATIONS

By Tiyamike Chisale The new Catholic Bishop in Malawi, Rt. Rev. Vincent Mwakhwawa has highlighted the need for the youth to respond to their vocations in accordance with what their hearts suggest. Bishop Mwakhwawa made the sentiments on Sunday 28th January 2023 at St. Paul Parish in Nkhotakota during his thanksgiving Mass at his home… Continue reading BISHOP MWAKHWAWA ENTREATS THE YOUTH TO RESPOND TO THEIR VOCATIONS