Achinyamata mu Arkidayosizi ya Lilongwe, apemphedwa kuti akuyenera kugwiritsa ntchito mwayi komanso kupanga ziganizo zoyenera pa momwe angatumikire Mulungu kudzera mmayitanidwe awo. Ambuye George Desmond Tambala a Arkidayosizi ya Lilongwe, ndiomwe apeleka pempholi lero pa 09 March 2025 ku Parish ya St. Mathias (Lumbadzi) pa mwambo wa nsembe ya Misa yotsekulira zochitikachitika za tsiku la… Continue reading “Achinyamata Asinkhesinkhe za Mayitanidwa Awo; Lero osati mawa,” Ambuye George Tambala
“Achinyamata Asinkhesinkhe za Mayitanidwa Awo; Lero osati mawa,” Ambuye George Tambala
